Deuteronomo 29:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Cholinga chake nʼchakuti lero akupangeni kuti mukhale anthu ake+ komanso kuti iye akhale Mulungu wanu,+ mogwirizana ndi zimene anakulonjezani ndiponso mogwirizana ndi zimene analumbira kwa makolo anu, Abulahamu,+ Isaki+ ndi Yakobo.+
13 Cholinga chake nʼchakuti lero akupangeni kuti mukhale anthu ake+ komanso kuti iye akhale Mulungu wanu,+ mogwirizana ndi zimene anakulonjezani ndiponso mogwirizana ndi zimene analumbira kwa makolo anu, Abulahamu,+ Isaki+ ndi Yakobo.+