Deuteronomo 29:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Koma ngati wina wamva mawu a lumbiro ili nʼkulankhula modzitama mumtima mwake kuti, ‘Ndikhala ndi mtendere ngakhale kuti ndikuyendabe motsatira zofuna za mtima wanga,’ zimene zidzachititse kuti aliyense woyandikana naye* awonongedwe,
19 Koma ngati wina wamva mawu a lumbiro ili nʼkulankhula modzitama mumtima mwake kuti, ‘Ndikhala ndi mtendere ngakhale kuti ndikuyendabe motsatira zofuna za mtima wanga,’ zimene zidzachititse kuti aliyense woyandikana naye* awonongedwe,