Deuteronomo 29:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Yehova sadzafuna kukhululukira munthu woteroyo.+ Mʼmalomwake, mkwiyo waukulu wa Yehova udzamuyakira, ndipo matemberero onse amene alembedwa mʼbuku ili adzamugwera,+ ndipo Yehova adzachotseratu dzina la munthuyo pansi pa thambo.
20 Yehova sadzafuna kukhululukira munthu woteroyo.+ Mʼmalomwake, mkwiyo waukulu wa Yehova udzamuyakira, ndipo matemberero onse amene alembedwa mʼbuku ili adzamugwera,+ ndipo Yehova adzachotseratu dzina la munthuyo pansi pa thambo.