-
Deuteronomo 29:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Kenako Yehova adzamupatula pa mafuko onse a Isiraeli kuti amubweretsere tsoka, mogwirizana ndi matemberero onse amene adzagwere anthu ophwanya pangano limene lalembedwa mʼbuku la Chilamulo ili.
-