Deuteronomo 29:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Zitatero mkwiyo wa Yehova unayakira dziko limeneli ndipo analibweretsera matemberero onse amene analembedwa mʼbuku ili.+
27 Zitatero mkwiyo wa Yehova unayakira dziko limeneli ndipo analibweretsera matemberero onse amene analembedwa mʼbuku ili.+