Deuteronomo 29:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Choncho Yehova anawazula mʼdziko lawo atapsa mtima,+ ali ndi ukali ndiponso mkwiyo waukulu nʼkuwapititsa kudziko lina, kumene ali lero.’+
28 Choncho Yehova anawazula mʼdziko lawo atapsa mtima,+ ali ndi ukali ndiponso mkwiyo waukulu nʼkuwapititsa kudziko lina, kumene ali lero.’+