Deuteronomo 29:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Yehova Mulungu wathu+ amadziwa zinthu zonse zobisika, koma amaulula zinthu kwa ifeyo komanso kwa zidzukulu zathu ku mibadwomibadwo, kuti titsatire mawu onse a Chilamulo ichi.”+ Deuteronomo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 29:29 Nsanja ya Olonda,5/15/1987, tsa. 315/15/1986, ptsa. 9-10
29 Yehova Mulungu wathu+ amadziwa zinthu zonse zobisika, koma amaulula zinthu kwa ifeyo komanso kwa zidzukulu zathu ku mibadwomibadwo, kuti titsatire mawu onse a Chilamulo ichi.”+