Deuteronomo 30:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndiyeno Yehova Mulungu wanu adzabweretsa matemberero onsewa pa adani anu, amene ankadana nanu komanso kukuzunzani.+
7 Ndiyeno Yehova Mulungu wanu adzabweretsa matemberero onsewa pa adani anu, amene ankadana nanu komanso kukuzunzani.+