Deuteronomo 30:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Chifukwa pa nthawiyo mudzamvera mawu a Yehova Mulungu wanu ndi kusunga malamulo komanso malangizo ake amene analembedwa mʼbuku ili la Chilamulo, ndipo mudzabwerera kwa Yehova Mulungu wanu ndi mtima wanu wonse komanso moyo wanu wonse.+
10 Chifukwa pa nthawiyo mudzamvera mawu a Yehova Mulungu wanu ndi kusunga malamulo komanso malangizo ake amene analembedwa mʼbuku ili la Chilamulo, ndipo mudzabwerera kwa Yehova Mulungu wanu ndi mtima wanu wonse komanso moyo wanu wonse.+