Deuteronomo 30:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Lamulo limene ndikukupatsani leroli si lovuta kwa inu kulitsatira, ndipo silili poti simungathe kulipeza.*+ Deuteronomo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 30:11 Nsanja ya Olonda,11/1/2009, tsa. 31
11 Lamulo limene ndikukupatsani leroli si lovuta kwa inu kulitsatira, ndipo silili poti simungathe kulipeza.*+