Deuteronomo 31:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kenako Yehova anauza Mose kuti: “Taona, nthawi yoti ufe yayandikira.+ Itana Yoswa, ndipo mukaime pachihema chokumanako kuti ndikamuike kukhala mtsogoleri.”+ Choncho Mose ndi Yoswa anapita nʼkukaima pachihema chokumanako.
14 Kenako Yehova anauza Mose kuti: “Taona, nthawi yoti ufe yayandikira.+ Itana Yoswa, ndipo mukaime pachihema chokumanako kuti ndikamuike kukhala mtsogoleri.”+ Choncho Mose ndi Yoswa anapita nʼkukaima pachihema chokumanako.