Deuteronomo 31:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Tsopano mulembe nyimbo iyi+ nʼkuphunzitsa Aisiraeli.+ Muwaphunzitse* nyimbo imeneyi kuti ikhale mboni yanga pamaso pa Aisiraeliwo.+
19 Tsopano mulembe nyimbo iyi+ nʼkuphunzitsa Aisiraeli.+ Muwaphunzitse* nyimbo imeneyi kuti ikhale mboni yanga pamaso pa Aisiraeliwo.+