Deuteronomo 31:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 “Tengani buku ili la Chilamulo+ ndipo muliike pambali pa likasa+ la pangano la Yehova Mulungu wanu, ndipo lidzakhala mboni ya Mulungu yokutsutsani. Deuteronomo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 31:26 Nsanja ya Olonda,7/15/1990, tsa. 28
26 “Tengani buku ili la Chilamulo+ ndipo muliike pambali pa likasa+ la pangano la Yehova Mulungu wanu, ndipo lidzakhala mboni ya Mulungu yokutsutsani.