-
Deuteronomo 32:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Malangizo anga adzagwa ngati mvula,
Mawu anga adzatsika ngati mame,
Ngati mvula yowaza pa udzu,
Ngatinso mvula yamphamvu pazomera.
-