Deuteronomo 32:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Iwo ndi amene achita zinthu zoipa.+ Iwo si ana ake, ali ndi vuto ndi iwowo.+ Iwo ndi mʼbadwo wopotoka maganizo komanso wachinyengo!+ Deuteronomo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 32:5 Nsanja ya Olonda,12/15/1988, tsa. 10
5 Iwo ndi amene achita zinthu zoipa.+ Iwo si ana ake, ali ndi vuto ndi iwowo.+ Iwo ndi mʼbadwo wopotoka maganizo komanso wachinyengo!+