Deuteronomo 32:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Anamupeza mʼdziko lachipululu,+Mʼchipululu chopanda kanthu, molira zilombo.+ Anamuzungulira kuti amuteteze, anamusamalira,+Ndipo anamuteteza ngati mwana wa diso lake.+
10 Anamupeza mʼdziko lachipululu,+Mʼchipululu chopanda kanthu, molira zilombo.+ Anamuzungulira kuti amuteteze, anamusamalira,+Ndipo anamuteteza ngati mwana wa diso lake.+