Deuteronomo 32:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndi Yehova yekha amene anapitiriza kumutsogolera,*+Panalibe mulungu wachilendo amene anali naye.+ Deuteronomo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 32:12 Nsanja ya Olonda,10/1/2001, tsa. 96/15/2001, tsa. 26