Deuteronomo 32:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Iwo ankapereka nsembe kwa ziwanda, osati kwa Mulungu.+Anapereka nsembe kwa milungu imene sankaidziwa,Kwa milungu yatsopano yongobwera kumene,Komanso kwa milungu imene makolo anu sankaidziwa.
17 Iwo ankapereka nsembe kwa ziwanda, osati kwa Mulungu.+Anapereka nsembe kwa milungu imene sankaidziwa,Kwa milungu yatsopano yongobwera kumene,Komanso kwa milungu imene makolo anu sankaidziwa.