Deuteronomo 32:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Yehova ataona zimenezi anawakana+Chifukwa chakuti ana ake aamuna ndi aakazi anamukhumudwitsa.