Deuteronomo 32:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Kunja, lupanga lidzawasandutsa anamfedwa.+Mʼnyumba, anthu adzagwidwa ndi mantha+Zimenezi zidzachitikira mnyamata, namwali,Mwana wamngʼono ndi munthu wa imvi.+
25 Kunja, lupanga lidzawasandutsa anamfedwa.+Mʼnyumba, anthu adzagwidwa ndi mantha+Zimenezi zidzachitikira mnyamata, namwali,Mwana wamngʼono ndi munthu wa imvi.+