Deuteronomo 32:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Chifukwa thanthwe lawo si lofanana ndi Thanthwe lathu,+Ndipo adani athu akudziwa bwino zimenezi.+