Deuteronomo 32:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Onani tsopano kuti ndine Mulungu,+Ndipo palibe Mulungu wina koma ine ndekha.+ Ndimapha komanso ndimapereka moyo.+ Ndimavulaza,+ ndipo ndidzachiritsa,+Palibe aliyense amene angapulumutse munthu mʼdzanja langa.+
39 Onani tsopano kuti ndine Mulungu,+Ndipo palibe Mulungu wina koma ine ndekha.+ Ndimapha komanso ndimapereka moyo.+ Ndimavulaza,+ ndipo ndidzachiritsa,+Palibe aliyense amene angapulumutse munthu mʼdzanja langa.+