-
Deuteronomo 32:42Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
42 Ndidzaledzeretsa mivi yanga ndi magazi,
Ndipo lupanga langa lidzadya nyama,
Ndi magazi a anthu ophedwa komanso ogwidwa,
Ndiponso mitu ya atsogoleri a adani.’
-