Deuteronomo 32:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 anawauza kuti: “Ganizirani mofatsa mawu onse okuchenjezani amene ndikulankhula nanu lero,+ kuti muuze ana anu kuti azionetsetsa kuti akuchita zimene mawu onse a Chilamulo ichi akunena.+ Deuteronomo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 32:46 Nsanja ya Olonda,10/15/2001, tsa. 198/15/1988, ptsa. 10-12
46 anawauza kuti: “Ganizirani mofatsa mawu onse okuchenjezani amene ndikulankhula nanu lero,+ kuti muuze ana anu kuti azionetsetsa kuti akuchita zimene mawu onse a Chilamulo ichi akunena.+