Deuteronomo 32:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Chifukwa amenewa si mawu opanda pake kwa inu, koma angakuthandizeni kukhala ndi moyo.+ Mukamatsatira mawu amenewa mudzakhala ndi moyo wautali mʼdziko limene mukuwoloka Yorodano kuti mukalitenge kukhala lanu.” Deuteronomo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 32:47 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),2/2023, tsa. 3 Nsanja ya Olonda,4/15/2008, ptsa. 5-6
47 Chifukwa amenewa si mawu opanda pake kwa inu, koma angakuthandizeni kukhala ndi moyo.+ Mukamatsatira mawu amenewa mudzakhala ndi moyo wautali mʼdziko limene mukuwoloka Yorodano kuti mukalitenge kukhala lanu.”