Deuteronomo 33:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Tsopano awa ndi madalitso amene Mose, munthu wa Mulungu woona, ananena asanafe kuti Aisiraeli adzalandira.+
33 Tsopano awa ndi madalitso amene Mose, munthu wa Mulungu woona, ananena asanafe kuti Aisiraeli adzalandira.+