Deuteronomo 33:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Iye ananena kuti Yuda adzalandira madalitso otsatirawa:+ “Inu Yehova, imvani mawu a Yuda,+Ndipo mumubwezere kwa anthu ake. Iye wateteza* zinthu zake ndi manja ake,Mumuthandize kulimbana ndi adani ake.”+
7 Iye ananena kuti Yuda adzalandira madalitso otsatirawa:+ “Inu Yehova, imvani mawu a Yuda,+Ndipo mumubwezere kwa anthu ake. Iye wateteza* zinthu zake ndi manja ake,Mumuthandize kulimbana ndi adani ake.”+