Deuteronomo 33:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ponena za Levi anati:+ “Tumimu ndi Urimu wanu*+ ndi za munthu wokhulupirika kwa inu,+Amene munamuyesa pa Masa.+ Munayamba kulimbana naye pafupi ndi madzi a ku Meriba.+
8 Ponena za Levi anati:+ “Tumimu ndi Urimu wanu*+ ndi za munthu wokhulupirika kwa inu,+Amene munamuyesa pa Masa.+ Munayamba kulimbana naye pafupi ndi madzi a ku Meriba.+