Deuteronomo 33:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Munthu amene anauza bambo ndi mayi ake kuti, ‘Sindinasonyeze kuti ndikuwalabadira.’ Ngakhale abale ake sanawasamale,+Ndipo ana ake anakhala ngati sakuwadziwa. Chifukwa anatsatira mawu anu,Ndipo anasunga pangano lanu.+
9 Munthu amene anauza bambo ndi mayi ake kuti, ‘Sindinasonyeze kuti ndikuwalabadira.’ Ngakhale abale ake sanawasamale,+Ndipo ana ake anakhala ngati sakuwadziwa. Chifukwa anatsatira mawu anu,Ndipo anasunga pangano lanu.+