Deuteronomo 33:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Amenewa azilangiza Yakobo pa zigamulo zanu+Ndi Isiraeli mʼChilamulo chanu.+ Azipereka nsembe zofukiza kuti zikhale kafungo kosangalatsa kwa inu,*+Ndi nsembe yathunthu paguwa lanu lansembe.+
10 Amenewa azilangiza Yakobo pa zigamulo zanu+Ndi Isiraeli mʼChilamulo chanu.+ Azipereka nsembe zofukiza kuti zikhale kafungo kosangalatsa kwa inu,*+Ndi nsembe yathunthu paguwa lanu lansembe.+