Deuteronomo 33:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ponena za Benjamini anati:+ “Wokondedwa wa Yehova azikhala wotetezedwa ndi iye,Pamene akumuteteza tsiku lonse,Iye adzakhala pakati pa mapewa ake.”
12 Ponena za Benjamini anati:+ “Wokondedwa wa Yehova azikhala wotetezedwa ndi iye,Pamene akumuteteza tsiku lonse,Iye adzakhala pakati pa mapewa ake.”