Deuteronomo 33:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ponena za Yosefe anati:+ “Dziko lake lidalitsidwe ndi Yehova.+Lidalitsidwe ndi zinthu zabwino kwambiri zakumwamba,Ndi mame komanso madzi ochokera mu akasupe a pansi pa nthaka.+
13 Ponena za Yosefe anati:+ “Dziko lake lidalitsidwe ndi Yehova.+Lidalitsidwe ndi zinthu zabwino kwambiri zakumwamba,Ndi mame komanso madzi ochokera mu akasupe a pansi pa nthaka.+