Deuteronomo 33:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Adzaitanira mitundu ya anthu kuphiri. Kumeneko adzapereka nsembe zachilungamo. Chifukwa adzatenga chuma* kuchokera pa chuma chochuluka cha mʼnyanja,Ndi chuma chobisika chamumchenga.”
19 Adzaitanira mitundu ya anthu kuphiri. Kumeneko adzapereka nsembe zachilungamo. Chifukwa adzatenga chuma* kuchokera pa chuma chochuluka cha mʼnyanja,Ndi chuma chobisika chamumchenga.”