Deuteronomo 33:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ponena za Nafitali anati:+ “Nafitali wakhutira chifukwa chovomerezedwa,Ndipo madalitso a Yehova amuchulukira. Tenga chigawo chakumadzulo ndi kumʼmwera.”
23 Ponena za Nafitali anati:+ “Nafitali wakhutira chifukwa chovomerezedwa,Ndipo madalitso a Yehova amuchulukira. Tenga chigawo chakumadzulo ndi kumʼmwera.”