Deuteronomo 33:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Isiraeli adzakhala motetezeka,Kasupe wa Yakobo adzakhala motetezeka,Mʼdziko lokhala ndi chakudya komanso vinyo watsopano,+Limene kumwamba kwake kudzagwetsa mame.+
28 Isiraeli adzakhala motetezeka,Kasupe wa Yakobo adzakhala motetezeka,Mʼdziko lokhala ndi chakudya komanso vinyo watsopano,+Limene kumwamba kwake kudzagwetsa mame.+