Deuteronomo 34:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kenako Mose mtumiki wa Yehova anafera pamenepo mʼdziko la Mowabu, mogwirizana ndi zimene Yehova ananena.+
5 Kenako Mose mtumiki wa Yehova anafera pamenepo mʼdziko la Mowabu, mogwirizana ndi zimene Yehova ananena.+