Deuteronomo 34:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mose anamwalira ali ndi zaka 120.+ Pa nthawiyo maso ake ankaonabe bwinobwino ndipo anali adakali ndi mphamvu. Deuteronomo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 34:7 Nsanja ya Olonda,12/15/1986, tsa. 30
7 Mose anamwalira ali ndi zaka 120.+ Pa nthawiyo maso ake ankaonabe bwinobwino ndipo anali adakali ndi mphamvu.