Yoswa 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ukhale wolimba mtima ndipo uchite zinthu mwamphamvu,+ chifukwa iweyo ndi amene utsogolere anthuwa kuti akatenge dziko limene ndinalumbira kwa makolo awo kuti ndidzawapatsa.+
6 Ukhale wolimba mtima ndipo uchite zinthu mwamphamvu,+ chifukwa iweyo ndi amene utsogolere anthuwa kuti akatenge dziko limene ndinalumbira kwa makolo awo kuti ndidzawapatsa.+