Yoswa 1:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Tidzamvera chilichonse chimene mungatiuze ngati mmene tinkachitira ndi Mose. Yehova Mulungu wanu akhale nanu ngati mmene anakhalira ndi Mose.+
17 Tidzamvera chilichonse chimene mungatiuze ngati mmene tinkachitira ndi Mose. Yehova Mulungu wanu akhale nanu ngati mmene anakhalira ndi Mose.+