Yoswa 1:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Munthu aliyense wophwanya dala malamulo anu, ndi wosamvera mawu anu pa chilichonse chimene mungamulamule, aphedwe.+ Inuyo mukhale wolimba mtima ndipo muchite zinthu mwamphamvu.”+
18 Munthu aliyense wophwanya dala malamulo anu, ndi wosamvera mawu anu pa chilichonse chimene mungamulamule, aphedwe.+ Inuyo mukhale wolimba mtima ndipo muchite zinthu mwamphamvu.”+