-
Yoswa 2:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Tsopano, chonde lumbirani pamaso pa Yehova, kuti chifukwa choti ndakusonyezani chikondi chokhulupirika, inunso mudzasonyeze anthu a mʼbanja la bambo anga chikondi chokhulupirika, ndipo mundipatse chizindikiro chodalirika.
-