Yoswa 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Amunawo anayankha kuti: “Tikadzapanda kusunga lonjezo lathu, ifeyo tidzafe mʼmalo mwa inu. Mukapanda kuulula nkhaniyi, Yehova akadzatipatsa dzikoli, ifenso tidzakusonyezani kukoma mtima* ndipo tidzakhala okhulupirika.”
14 Amunawo anayankha kuti: “Tikadzapanda kusunga lonjezo lathu, ifeyo tidzafe mʼmalo mwa inu. Mukapanda kuulula nkhaniyi, Yehova akadzatipatsa dzikoli, ifenso tidzakusonyezani kukoma mtima* ndipo tidzakhala okhulupirika.”