Yoswa 2:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 ngati pobwera tidzapeza utamangirira chingwe chofiirachi pawindo limene watitulutsirapoli. Uuze bambo ako, mayi ako, azichimwene ako, azichemwali ako ndi onse a mʼbanja la bambo ako kuti adzakhale mʼnyumba mwakomu.+
18 ngati pobwera tidzapeza utamangirira chingwe chofiirachi pawindo limene watitulutsirapoli. Uuze bambo ako, mayi ako, azichimwene ako, azichemwali ako ndi onse a mʼbanja la bambo ako kuti adzakhale mʼnyumba mwakomu.+