-
Yoswa 2:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Aliyense amene adzatuluke mʼnyumba yako kupita panja, magazi ake adzakhala pamutu pake ndipo ife tidzakhala opanda mlandu. Koma aliyense amene adzakhalebe nawe mʼnyumbamu akadzaphedwa, magazi ake adzakhala pamutu pathu.
-