Yoswa 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndipo Yehova anauza Yoswa kuti: “Lero ndiyamba kukulemekeza pamaso pa Aisiraeli onse+ nʼcholinga choti adziwe kuti ndidzakhala nawe+ ngati mmene ndinkachitira ndi Mose.+
7 Ndipo Yehova anauza Yoswa kuti: “Lero ndiyamba kukulemekeza pamaso pa Aisiraeli onse+ nʼcholinga choti adziwe kuti ndidzakhala nawe+ ngati mmene ndinkachitira ndi Mose.+