Yoswa 4:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Miyalayo idzakhala chizindikiro kwa inu. Ana anu* akamadzafunsa mʼtsogolo muno kuti, ‘Kodi miyalayi ndi ya chiyani?’+ Yoswa Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:6 Nsanja ya Olonda,12/15/1986, tsa. 16
6 Miyalayo idzakhala chizindikiro kwa inu. Ana anu* akamadzafunsa mʼtsogolo muno kuti, ‘Kodi miyalayi ndi ya chiyani?’+