-
Yoswa 4:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Choncho Aisiraeliwo anachita zimene Yoswa anawalamula. Anapita pakati pa mtsinje wa Yorodano, ndipo anakanyamula miyala 12 mogwirizana ndi chiwerengero cha mafuko a Aisiraeli, ngati mmene Yehova analamulira Yoswa. Ananyamula miyalayo nʼkupita nayo kumalo amene anagona.
-