Yoswa 4:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pa tsikuli, Yehova anachititsa Aisiraeli onse kuona kuti Yoswa ndi mtsogoleri wamkulu,+ ndipo anayamba kumulemekeza* kwambiri masiku onse a moyo wake ngati mmene ankalemekezera Mose.+
14 Pa tsikuli, Yehova anachititsa Aisiraeli onse kuona kuti Yoswa ndi mtsogoleri wamkulu,+ ndipo anayamba kumulemekeza* kwambiri masiku onse a moyo wake ngati mmene ankalemekezera Mose.+