-
Yoswa 5:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Atamaliza kudula amuna onse, aliyense anakhalabe muhema wake pamsasapo mpaka atachira.