Yoswa 5:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Aisiraeliwo anakhalabe ku Giligala ndipo anachita Pasika madzulo pa tsiku la 14 la mweziwo,+ mʼchipululu cha Yeriko.
10 Aisiraeliwo anakhalabe ku Giligala ndipo anachita Pasika madzulo pa tsiku la 14 la mweziwo,+ mʼchipululu cha Yeriko.